Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 35:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anampatsa Yakobo milungu yacilendo yonse inali m'manja mwao, ndi mphete zinali m'makutu mwao: ndipo Yakobo anazibisa pansi pa mtengo wathundu unali pa Sekemu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 35

Onani Genesis 35:4 nkhani