Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 34:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakumva ico ana ace amuna a Yakobo anabwera pocokera kudambo: amunawo ndipo anaphwetekwa mtima, nakwiya kwambiri, cifukwa iyeyo anacita copusa coipira Israyeli pakugona ndi mwana wamkazi wa Yakobo; ndico cosayenera kucita.

Werengani mutu wathunthu Genesis 34

Onani Genesis 34:7 nkhani