Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 34:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anati kwa Simeoni ndi Levi, Mwaodisautsa ndi kundinunkhitsa ine mwa anthu okhala m'dzikomu, mwa Akanani ndi mwa Aperezi; ndipo ine ndine wa anthu owerengeka, adzandisonkhanira ine ndi kundikantha: ndipo ndidzapasulidwa ine ndi a pa nyumba yanga.

Werengani mutu wathunthu Genesis 34

Onani Genesis 34:30 nkhani