Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 34:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo tidzakupatsani inu ana athu akazi, ndipo tidzadzitengera ana anu akazi, ndipo tidzakhala pamodzi ndi inu, ndi kukhala mtundu umodzi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 34

Onani Genesis 34:16 nkhani