Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 33:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anankabe ulendo wace ku Sukoti, namanga nyumba yace pamenepo, namanga makola a zoweta zace: cifukwa cace dzina lace la kumeneko ndi Sukoti.

Werengani mutu wathunthu Genesis 33

Onani Genesis 33:17 nkhani