Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 33:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mbuyanga atsogoleretu kapolo wace, ndipo ine ndidzazitsogolera pango'no-pang'ono monga mwa mayendedwe a zoweta ziri pamaso panga, ndi monga mwa mayendedwe a ana, mpaka ndifike kwa mbuyanga ku Seiri.

Werengani mutu wathunthu Genesis 33

Onani Genesis 33:14 nkhani