Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 32:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ana a Israyeli samadya ntsempha ya thako iri pa nsukunyu ya ncafu kufikira lero: cifukwa anakhudza nsukunyu ya ncafu ya Yakobo pa ntsempha ya thako.

Werengani mutu wathunthu Genesis 32

Onani Genesis 32:32 nkhani