Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 32:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiponso muziti, Ndiponso, taonani, kapolo wanu Yakobo ali pambuyo pathu, Pakuti anati, Ndidzampembedzera iye ndi mphatso imene ipita patsogolo panga, pambuyo pace ndidzaona nkhope yace; kapena adzandilandira ine.

Werengani mutu wathunthu Genesis 32

Onani Genesis 32:20 nkhani