Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 31:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anapereka nsembe paphiripo, naitana abale ace kuti adye cakudya; ndipo anadya cakudya, nagona paphiripo usiku wonse.

Werengani mutu wathunthu Genesis 31

Onani Genesis 31:54 nkhani