Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 31:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Labani anakomana naye Yakobo. Ndipo Yakobo anamanga hema wace m'phirimo: ndipo Labani ndi abale ace anamanga m'phiri la Gileadi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 31

Onani Genesis 31:25 nkhani