Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 31:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali potenga mabere ziwetozo, ine ndinatukula maso anga, ndipo ndinapenya m'kulota, taonani, atonde okwera ziweto anali amipyololo-mipyololo, amathotho-mathotho, ndi amaanga-maanga.

Werengani mutu wathunthu Genesis 31

Onani Genesis 31:10 nkhani