Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 31:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yakobo afuna kwao nathawa nazo zace, Ndipo anamva mau a ana ace a Labani kuti, Yakobo watenga zonse za atate wathu; m'zinthu zinali za atate wathu wapeza iye cuma ici conse.

Werengani mutu wathunthu Genesis 31

Onani Genesis 31:1 nkhani