Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 30:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo analekanitsa ana a nkhosa naziika nkhope za zoweta kuti ziyang'anire zamipyololo-mipyololo, ndi zakuda zonse za m'zoweta za Labani, ndipo anaika magulu ace pa okha; sanaziika pa zoweta za Labani.

Werengani mutu wathunthu Genesis 30

Onani Genesis 30:40 nkhani