Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 30:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anatenga nthyole za mtengo wowisi walibne, ndi za mtengo wakatungurume, ndi za mtengo waarimoni, nakupula m'menemo mizere yoyera, naonetsa moyera mwa m'nthyolemo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 30

Onani Genesis 30:37 nkhani