Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 30:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lomwelo Labani anacotsa atonde amene anali amipyololo-mipyololo ndi amathotho-mathotho, ndi mbuzi zazikazi zinali zamaanga-maanga ndi zamathotho-mathotho zonse zinali zoyera pang'ono, ndi zakuda zonse za nkhosa, napatsa m'dzanja la ana ace amuna.

Werengani mutu wathunthu Genesis 30

Onani Genesis 30:35 nkhani