Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 3:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kwa Adamu ndipo anati, Cifukwa kuti wamvera mau a mkazi wako, nudya za mtengo umene ndinakuuza iwe kuti, Usadyeko; nthaka ikhale yotembereredwa cifukwa ca iwe; m'kusauka udzadyako masiku onse a moyo wako:

Werengani mutu wathunthu Genesis 3

Onani Genesis 3:17 nkhani