Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 29:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenganso pakati, nabala mwana wamwamuna nati, Cifukwa anamva Yehova kuti anandida ine, anandipatsa ine mwana wamwamuna uyunso; ndipo anamucha dzina lace Simeoni.

Werengani mutu wathunthu Genesis 29

Onani Genesis 29:33 nkhani