Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 29:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo analowanso kwa Rakele, namkondanso Rakele kopambana Leya, namtumikira Labani zaka zisanu ndi ziwiri zinanso.

Werengani mutu wathunthu Genesis 29

Onani Genesis 29:30 nkhani