Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 29:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali pamene Yakobo anaona Rakele, mwana wamkazi wa Labani, mlongo wace wa amace, ndi nkhosa za Labani mlongo wace wa amace, Yakobo anayandikira nagubuduza kuucotsa mwala pacitsime, nazimwetsa zoweta za Labani, mlongo wace wa amace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 29

Onani Genesis 29:10 nkhani