Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 27:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati Rebeka kwa Isake, Ndalema moyo wanga cifukwa ca aria akazi a Heti: akatenga Yakobo mkazi wa ana akazi a Heti, onga ana akazi a m'dziko lino, moyo wanga udzandikhalira ine bwanji?

Werengani mutu wathunthu Genesis 27

Onani Genesis 27:46 nkhani