Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 27:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Esau anati kwa atate wace, Kodi muli nao mdalitso umodzi wokha, atate wanga? Mundidalitse ine, inenso, atate wanga, Ndipo Esau anakweza mau ace nalira.

Werengani mutu wathunthu Genesis 27

Onani Genesis 27:38 nkhani