Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 27:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati, Kodi si ndico cifukwa anamucha dzina lace Yakobo? kuti wandinyenga ine kawiri aka; analanda ukulu wanga ndipo taonani, tsopano walanda mdalitso wanga. Ndipo anati, Kodi smunandisungira ine mdalitso?

Werengani mutu wathunthu Genesis 27

Onani Genesis 27:36 nkhani