Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 27:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu akutumikire iwe,Mitundu ikuweramire iwe;Ucite ufumu pa abale ako,Ana a amako akuweramire iwe;Wotemberereka ali yense akutemberera iwe,Wodalitsika ali yense akudalitsa iwe.

Werengani mutu wathunthu Genesis 27

Onani Genesis 27:29 nkhani