Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 26:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abimeleke anamuitana Isake nati, Taona, uyo ndi mkazi wako ndithu: kodi bwanji unati, Ndiye mlongo wanga? Ndipo Isake anati kwa iye, Cifukwa ndinati, Ndingafe cifukwa ca iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 26

Onani Genesis 26:9 nkhani