Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 26:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo anthu a kumeneko anamfunsa iye za mkazi wace; ndipo iye anati, diye mlongowanga: cifukwa kuti anaopa kunena, Mkazi wanga; anati, anthu a kumeneko angandiphe ine cifukwa ca Rebeka; popeza anali wokongola pakumuona.

Werengani mutu wathunthu Genesis 26

Onani Genesis 26:7 nkhani