Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 26:34-35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

34. Pamene Esau anali wa zaka makumi anai, anakwatira Yuditi mwana wamkazi wa Beeri Mhiti, ndi Basemati mwana wamkazi wa Elone Mhiti:

35. ndipo iwo anapweteka mtima wa Isake ndi wa Rebeka.

Werengani mutu wathunthu Genesis 26