Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 26:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anamuonekera iye usiku womwewo, nati, Ine dine Mulungu wa Abrahamu atate wako; usaope, cifukwa kuti Ine ndiri ndi iwe, ndipo ndidzakudalitsa iwe, ndi kucurukitsa mbeu zako, cifukwa ca Abrahamu kapolo wanga.

Werengani mutu wathunthu Genesis 26

Onani Genesis 26:24 nkhani