Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 26:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Isake anafukulanso zitsime za madzi, anazikumba masiku a Abrahamu atate wace; cifukwa kuti Afilisti anazitseka atafa Abrahamu: ndipo anazicha maina monga maina omwe anazicha atate wace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 26

Onani Genesis 26:18 nkhani