Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 26:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali njala padzikopo, yoyenjezeka ndi njala yoyamba ija imene inali masiku a Abrahamu, ndipo Isake ananka kwa Abimeleke mfumu ya Afilisti ku Gerari.

Werengani mutu wathunthu Genesis 26

Onani Genesis 26:1 nkhani