Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 25:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Abrahamu anatenga mkazi wina dzina lace Ketura.

2. Ndipo anambalira iye Zimerani ndi Yokesani ndi Medani, ndi Midyani, ndi Yisebaki, ndi Sua.

3. Ndipo Yokesani anabala Seba, ndi Dedani. Ana a Dedani ndi Aasuri, ndi Aletusi, ndi Aleumi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 25