Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 24:67 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Isake anamlowetsa mkaziyo m'hema wa amace Sara, namtenga Rebeka, nakhala iye mkazi wace; ndipo anamkonda iye; ndipo Isake anatonthozedwa mtima atafa amace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:67 nkhani