Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 24:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali zitatha kumwa ngamila, munthuyo anatenga mphete yagolidi ya kulemera kwace sekele latheka, ndi zingwinjiri ziwiri za m'manja ace, kulemera kwace masekele khumi a golidi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:22 nkhani