Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 23:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena kwa Efroni alinkumva anthu a m'dzikomo, kuti, Koma ngati ufuna, undimveretu ine: ndidzakupatsa iwe mtengo wace wa munda; uulandire kwa ine, ndipo ndidzaika wakufa wanga m'menemo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 23

Onani Genesis 23:13 nkhani