Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 23:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Efroni anakhala pakati pa ana a Heti: ndipo Efroni Mhiti anayankha Abrahamu alinkumva ana a Heti, onse amene analowa pa cipata ca mudzi wace, kuti,

Werengani mutu wathunthu Genesis 23

Onani Genesis 23:10 nkhani