Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 23:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Sara anali wa zaka zana limodzi kudza makumi awiri ndi zisanu ndi ziwiri: ndizo zaka za moyo wa Sara.

2. Ndipo Sara anafa m'Kiriyati-araba (ndiwo Hebroni), m'dziko la Kanani; ndipo Abrahamu anadza ku maliro a Sara, kuti amlire.

Werengani mutu wathunthu Genesis 23