Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 22:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kudalitsa ndidzakudalitsa iwe, kucurukitsa ndidzacurukitsa mbeu zako monga nyenyezi za kumwamba, monga mcenga wa m'mphepete mwa nyanja; ndipo mbeu zako zidzagonjetsa cipata ca adani ao;

Werengani mutu wathunthu Genesis 22

Onani Genesis 22:17 nkhani