Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 21:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace anati kwa Abrahamu, Cotsa mdzakazi uyo, ndi mwana wace wamwamuna; cifukwa mwana wa mdzakazi uyo sadzalowa m'nyumba pamodzi naye mwana wanga Isake.

Werengani mutu wathunthu Genesis 21

Onani Genesis 21:10 nkhani