Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi zomera zonse za m'munda zisanakhale m'dziko lapansi, ndiponso matherere onse a m'munda asanamere; cifukwa Yehova Mulungu sanabvumbitsire mvula pa dziko lapansi, ndipo panalibe munthu wakulima nthaka;

Werengani mutu wathunthu Genesis 2

Onani Genesis 2:5 nkhani