Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 19:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Fulumira, thawira kumeneko; pakuti sindithai kucita kanthu usadafike kumeneko. Cifukwa cace anacha dzina la mudziwo Zoari.

Werengani mutu wathunthu Genesis 19

Onani Genesis 19:22 nkhani