Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 18:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatukula maso ace, nayang'ana, taonani, anthu atatu anaima pandunji pace; pamene anaona iwo, anawathamangira kucoka ku khomo la hema kukakomana nao, nawerama pansi, nati,

Werengani mutu wathunthu Genesis 18

Onani Genesis 18:2 nkhani