Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 17:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzalimbitsa pangano langa ndi Ine ndi iwe pa mbeu zako za pambuyo pako m'mibadwo yao, kuti likhale pangano la nthawi zonse, kuti ndikhale Mulungu wako ndi wa mbeu zako za pambuyo pako.

Werengani mutu wathunthu Genesis 17

Onani Genesis 17:7 nkhani