Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 17:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abrahamu anatenga Ismayeli mwana wace ndi onse amene anabadwa m'nyumba mwace, ndi onse, amene anagulidwa ndi ndalama zace, amuna onse a mwa anthu a kunyumba kwace kwa Abrahamu, nadula khungu lao tsiku lomwelo, monga Mulungu ananena naye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 17

Onani Genesis 17:23 nkhani