Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 17:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anati, Koma Sara mkazi wako adzakubalira iwe mwana wamwamuna; ndipo udzamucha dzina lace Isake; ndipo ndidzalimbikitsa nave pangano langa, kuti likhale pangano la nthawi zonse, la ku mbeu zace za pambuyo pace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 17

Onani Genesis 17:19 nkhani