Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 15:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zitapita izo, mau a Yehova anadza kwa Abramu m'masomphenya, kuti, Usaope, Abramu, Ine ndine cikopa cako ndi mphotho yako yaikurukuru.

Werengani mutu wathunthu Genesis 15

Onani Genesis 15:1 nkhani