Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 14:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

iwo anathira nkhondo pa Bera mfumu ya Sodomu, ndi pa Birisa, mfumu ya Gomora, ndi pa Sinabi mfumu ya Adima, ndi pa Semebere mfumu ya Ziboimu, ndi pa mfumu ya Bela (kumeneko ndi ku Zoari).

Werengani mutu wathunthu Genesis 14

Onani Genesis 14:2 nkhani