Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 13:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anankabe ulendowace kucokera ku dziko la kumwera kunka ku Beteli, kufikira kumalo kumene kunali hema wace poyamba paja, pakati pa Beteli ndi Ai;

Werengani mutu wathunthu Genesis 13

Onani Genesis 13:3 nkhani