Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 13:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Abramu, atalekana naye Loti, Tukulatu maso ako, nuyang'anire kuyambira kumene uliko, kumpoto, ndi kumwela, ndi kum'mawa, ndi kumadzulo:

Werengani mutu wathunthu Genesis 13

Onani Genesis 13:14 nkhani