Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 12:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abramu anatenga Sarai mkazi wace, ndi Loti mwana wa mphwace, ndi cuma cao cimene anasonkhanitsa, ndi miyoyo imene anabala m'Harana; naturuka kunka ku dziko la Kanani, ndipo anadza ku dziko la Kanani.

Werengani mutu wathunthu Genesis 12

Onani Genesis 12:5 nkhani