Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 10:27-30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. ndi Hadorimu ndi Uzali, ndi Dikila;

28. ndi Obali, ndi Abimaele, ndi Sheva;

29. ndi Ofiri ndi Havila, ndi obabi; onse amenewa ndi ana a okitani.

30. Kwao kunayamba pa Mesa pakunka ku Sefere phiri la kum'mawa.

Werengani mutu wathunthu Genesis 10