Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 10:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mibadwo ya ana a Nowa, Semu, Hamu, ndi Yafeti, ndi iyi; kwa iwo ndipo kunabadwa ana amuna, citapita cigumula cija.

2. Ana amuna a Yafeti: Gomeri, ndi Magogi, ndi Madai, ndi Yavani, ndi Tubala, ndi Mesheki, ndi Tirasi,

Werengani mutu wathunthu Genesis 10